Cifra Club

Nizakupanga Ngozi

Ngozi Family

We don't have the chords for this song yet.

Pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu
Cifukwa ngati ulibe ulemu nizakupanga Ngozi
Ine ndikonda antu a ulemu
Cifukwa ine niziba kucaya tu mambama twabwino

Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu

Pobwela pa nyumba uyenela ku nkala ndi ulemu
Cifukwa bena sibafuna vo kambakamba
Vo kambakamba vi leta pamulomo
Cifukwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi

Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu

Peleka ulemu
Bena bacaya Ngozi yovuta
Kukopo
[?]

Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu

Pobwela pa nyumba panga uyenela ku nkala ndi ulemu
Cifukwa, ine sinifuna vo kambakamba
Vo kambakamba vi leta pamulomo
Cifukwa bena baziba kuyasha tukopo twa ngozi

Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu
Tiza cita cani
Kwa inu anzatu
Kuti mupeleke ulemu kwanzanu

Other videos of this song
    0 views

    Chord tuning

    Online tuner

    Ops (: Content available only in Portuguese.
    OK