Cifra Club

Ndiwe Wanga

Chex BT

We don't have the chords for this song yet.

É o King
Chex
Haaaaa, the only, the only

Ndiwe wekha, iwe wekha, ndiwe wanga

Ndiwe wanga, beby yanga, nkazi wanga
Baby ine ndimakonda iwe wekha
Baby ine ndimafuna iwe wekha
Love yanga ndimapatsa iwe wekha
Iwe ndiwe wanga wanga
Future Mother wa ana anga
Madamo a nyumba yanga

Iwe ndiwe wanga wanga
Future Mother wa ana anga
Madamo a nyumba yanga
Ndiwe wekha unatenga

Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga
(My love)
(My love)
(My love)
Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga
(My love)
(My love)
(My love)

Padziko assanje alipo ambiri
Tiye tikondane m'mene tililj
Iwe ndi ine tipangue mbiri, (huuuu mbiri)
Opanda iwe sinditha kukhala
Opanda iwe baby ine ndimamala
Zokamba kamba ossawavela
Kukhala ndiwe, baby ine ndimamala

Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga
(My love)
(My love)
(My love)
Ndiwe wekha iwe wekha ndiwe wanga
(My love)
(My love)
(My love)

Other videos of this song
    0 views

    Chord tuning

    Online tuner

    Ops (: Content available only in Portuguese.
    OK